12 TACC angónia

12  TACC angónia Ensinamentos da Bíblia e história

17/10/2022

Wakhungu kodi nkutsogolera wakhungu mzake

Aneba aja anatsagula wawo mpingo akuti ndi:
TISAMBE SAVES CHURCH.
koma abale inu....

Like page.....

17/10/2022

DAVITE: anapha goliyati.

SAMSON: Anapha nkango.

INE: Ndidapha mbewa

Nanga Inu munaphako chiyani????

Like Page....!

09/09/2022

______________________________
Brothers and sisters

Mumapephera inde , koma kodi mumamudziwa amene Anachotsa ntundu WA ana a Israel mudziko lá Egipto????
nAnga mumamudziwa amene anafa kamba kazolakwa zanthu koma lero Lino ali moyo????

Nkutheka Kuti munayamba nkale kumpepha mulungu Kuti akupatseni zosowa zanu, koma simulandila .
Vuto sikuti ndi mulungoyo aí koma ndi inu enuwakenu , mukuphonya pena pake, pakuti milungu ndi ambuye Alipo âmbiri koma kwa ife Ana a Israel , kuli mulungu m,modzi ndi ambuye m,modzi WA mpostolo .

Send a message to learn more

08/09/2022

Chikondi chamulungu.
❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️

Lero lino SUMADZIWA Kuti ungafike nthawi zino, koma tawona ,ndichikondi cha mpostolo wa ambuye wathu yesu cristo, uli ndi moyo...
Uli ndi zofooka zako ,ndipo mulungu amadziwa Zofooka zakozo , koma munkuyesetsa mulungu sakuwelengera zolakwa zako.

Search page... coment, like and share ku magrupo anu....

26/08/2022

Page iye, yapangilidwila onse Ana anyumba ya Israel, ndipo kungokwanitsa 30 like , ndipamene ntchito iyambike.

25/08/2022

________NDINKACHEDWA PATI_____

like page..

Maria kodi wadya kale nsima ija ? Awatu anali agogo ake kunfusa dzukulu wawo ngati wadya nsima, chifukwa pathawi yomwe ankaphika chakudya ndinkuti iye ali kudambo kochapa..
Mmmh ayi agogo sindinadye kale dikilani ndiyanike kaye zovalazi Kuti ndidye ,anayakha akumweturira .
Agogo: nde panga Changu, chifukwa azibale Ako sanadyeso shadreck, John komaso Esther ndi Marita, dele ndadya ndekha ineyo.
Maria: iii amadikila chiyani nanga?
Agogo: iiii ati amadikila iweyo, poti lero kuzachinyamata akaweluka mwansanga.
Chabwino agogo, apasono ndamaliza nditenge kaye chakudyacho, maria analowa nyumba nkutenga nsima ija ndikuika patebulo , atatha kukoza zonse anawaitana abale ake onse..atangomaliza kusamba m,manja, maria anayamba kulakhura yekhayekha avekele :

Nthupi langa lagwidwa tsemwe,ndikuva kutetha kwambiri, komaso mutu ukundiwawa kwambiri, kutsogolo kwanga ndikuwona kwaima anyamata 5 koma ali maliseche, ndipo ndiwotuwa kwambiri ngati Kuti atha sabata ziwiri osasamba, ndipo ntima wanga ukugunda kwambiri....
Azichemwali ake onse anangokhala ndi chidwi pazomwe ankakamba Maria.
Kenaka Maria anapumila m,mamba ndikudzati mpostolo wambuye wathu yesu cristo mwalorelanji Kuti zitelo,?
Nthawi yomweyo anangogwa pansi.
Azibale amaria anasiyiza kudya nkuyamba kulira uku John akuthamanga kukayitana agogo ake pakuti panthawiyi nkuti atapita kumadzi.........

Like page...
NKHANI imeneyi iyamba Sunday🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻🙏🏻

Endereço

Lifidzi
Tete

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando 12 TACC angónia publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Entre Em Contato Com A Universidade

Envie uma mensagem para 12 TACC angónia:

Atalhos

Compartilhar

Categoria