16/11/2022
Right by Dan wa haroon plz flow the page βββββ kufika apapa ndakomana nazo sichibwana ai km kumbali yanga ndimathokosa mulungu pondisindila Nyengo dzanga.. mwa anthu ochuluka amaganidza ngati nchuma ichi ndichagadzi km ai ndikulimbikila kwanga bs ndiposo ena ndikamaudxa kuti ndagulitsako madzila ndochi masuku ndizina zotero km paka pano Samakhulupililabe km chachikulu ndikukhulupilila mulungu ndithu kt mulungu ndie ndamene amasintha Nyengo zamunthu aliyese ..
Km chimene chimafunika ndikulupililo ndikulimbikala bs km ineo chinthu chimoz ndichime ndinali ndinabe mtima odalila km kulimbikila basi penapake mtima odalila siwabwino umangoononga nthawi pachabe malo moti upuche mwawenkha uku ukudikila kt mulungu apanga nawe chani mukulimbikila kwako kwaineo or anthu atanena motani ndimakhala ndilibe nazo nchito coz chilungamo ndikuchiziwa ndekha kuti ndikuchokela pati....
Km Pena umbawi umakupangitsa munthu kuganidza wrong ichi ndifukwa anthu ambili amalowelela chimene amafuna nditendele wadzachuma kt apedza zosowa dzawo km kunena zoona ndalama ndiyofunika ndthu ichi ndichifukwa anthu amakhala ali yakaliyali kufuna zinchito kmso kupanga ma business osiyanasiyana uku kumakhala kufuna tendele wasosowa dzawo koma anthu ena Amanena kuti munthu kuchita bwino zimakhala zakutundu km waineo ndikuti ndizabodxa coz kwatu kwaineo kunalibe or moxi anachitako bwino km uwu umakha daliso ochokela kwamulungu bs ndiposo mukhale ndichikhulupililo chakuti mulungu akalodza kuti uyu achite bwino zimachitika bs or adani ako atachita kudumba Malele km kuchita bwino kumakha kwakufikila bs ndie plz ikani chikuluphililo chanu mwa mulungu nthawi ndinyengo idxakwana..
Day ina nditakhala padeni ndikuonera TV ndinangolandila fon km akayimbayu anali dzanga amene ndinachedza nawo dzaka zambuyomu ine nditanga fon choyamba kuyakhula dzangayi anati kod anse ulipo kod ungandilole kuti tikumane ..... ine poti uyu adali dxanga ndidamuuza eya vuto palibe umaganidza ubwera liti pondiyankha anangoti mawa kod atabwera anandiudza zotani tiye tikumane mu next part inawo pls like the page kuti tipitilize bwino thanks guys πππππ